Owerengawe khala maso

Owerengawe khala maso Its all about sharing Gods words ...

10/12/2025
10/12/2025

MAU WOGONELA

Mukadzanena m'mtima mwanu, Amitundu awa andichurukira; ndikhoza bwanji kuwapitikitsa?18, Musamawaopa; mukumbukile bwino chimene Yehova Mulungu wanu anachitira Farao, ndi Aigupto onse.

DEUTERONOMO 7:17-18📖🛌
Tsiku lina inunso mudzaona zomwe anaona Farao ndi Aigupto onse, amawazuza ana a Mulungu kuwachita nkhanza momwe angathere koma tsiku linakwana, inunso lanu tsiku lidzakwana itini pheeeee, bapangani zimenezo mudzaona za kwa Farao, anthuwo mudzawapitikitsa bwanji? Pemphero nde chida chake amenewo mudzathana nawo or atachuluka bwanji mudzina la Mulungu adzalephera.
Mukhale ndi usiku wopambana nonse

https://youtu.be/qQP4TCWr2_4
10/12/2025

https://youtu.be/qQP4TCWr2_4

Enjoy the videos and music you love, upload original content, and share it all with friends, family, and the world on YouTube.

10/12/2025

Mmoyo Uno musasadzayembekezere Kuti Anthu adzakupatsani zabwino zokha zokha ..

✍️Nthawi zina mwachipongwe akhoza kukupatsani Mzimbe komano mulibe manu.
✍️ Kukupatsani nsapato mulibe Phazi.

Chilichonse Mwalandira Kwa anthu chipemphelereni Mulungu adzachitembenuza, kukhala madalitso Anu!

Mzimbeyo mukaidzala mudzagulitsa ndikugura packet ya Sugar.

Chotero amene amasintha nyengo Za Munthu Ndi Mulungu mwini wake.

Ndikutheka 2025, Mwalandira zipongwe Zambiri,

OSADANDAULA TILI NDI MULUNGU IFE!

âś…Mbuyomo anamukweza Yosefe kuchokera mudzenje kukafikira Ku Palace.Genesis 41:40
âś…Anamukweza Mefibiset kuchokera Ku Lodebala kukafika Ku Nyumba ya Chifumu Ku Yerusalemu. 2 Samuel 19:24-30.
âś…Anasintha nyengo za Estere mpakana Kukhala wokondedwa weni weni wa mfumu. Estere 5:2
âś…Anasintha nyengo za Mzimayi wadama kufikira anakhala wokhazikika.Yohani 8:11
âś…Anadalitsanso Yobu Ndi Chuma choposa choyamba chija komanso ana ena okongoka Yobu 42.

Onsewa Dziko linawapanga mistreat komano Mulungu Anasintha Nyengo zawo!!!

Ofunika kulapa Ndi kuyambanso kuyenda Ndi Mulungu.

copied

23/11/2025

*📖 MAU ALERO 📖📝Miyambo 4:23 Cinjiriza mtima wako koposa zonse uzisunga; Pakuti magwero a moyo aturukamo.* Kodi pa moyo wanu mumatchinjiriza ndi chiyani? Tisatchinjirize ntchito, banja, katundu, udindo, ndi china chili chonse chomwe tili nacho. Zonsezi mzachabe. Tiyeni titchinjirize mtimawu, chifukwa moyo wathu ukati watha, zokhumba za moyo wathu zathera pomwepo. Ambiri mmalo motchinjiriza mtima ndipomwe tikuononga, ena tikuikamo fodya, mowa, ufiti, nsanje, ndi zina zambiri zomwe Mulungu akudana nazo. Magwero a moyo amatuluka, ndiye mphweya. Tiyeni pomwe tili ndi moyo tiugwiritse ntchito moyenera. Tichite chifuniro cha Mulungu kuti titati tagona lero moyo winawo tikadzukire ku chipulumutso. Amen

21/11/2025

*MAWU ODZUKIRA*

*Lero tidzuke ndi mawu opezeka pa*

*Miyambo 4:23*

"Tchinjiriza mtima wako koposa zonse uzisunga; pakuti magwero amoyo atulukamo."

Mukhale ndi tsiku lopambana Ambuye akutsogoleleni.

𝗔𝗺𝗲𝗻.🙏

20/11/2025

MAU WODZUKILA MORNING WATCH

Ndidziwa ntchito zako(*taona, ndapatsa pamaso pako khomo lotseguka limene munthu sakhoza kusekapo)* Kuti uli nayo mphamvu pang'ano, ndipo unasunga mau anga, osakana dzina langa.

CHIBVUMBULUTSO 3:8📖🛏️
Koma anthu mukuyesetsa kufuna kutseka makomo azanu amene Mulungu anatsegula kale. tidzikhala ndi manyazi, ndi mantha ndi Mulungu tisatseke makomo azathu zimenso sizingatipindulire kuipa mtima kumangofuna zathu adzimvutika basi. koma Mulungu anatsegula kale Khomo.
Mukhale ndi tsiku lopambana nonse.

17/08/2024

happy Sabbath day saints .

21/05/2024

*SEED FOR LIFE*
For God has not called us to impurity, but to holiness. • 1 Thessalonians 4:7

Life is a gift of God. Our bodies have been given us to use in God’s service, and He desires that we shall care for and appreciate them... We are possessed of physical as well as mental faculties... Our bodies must be kept in the best possible condition physically and under the most spiritual influences... Our bodies belong to God. He paid the price of redemption for the body as well as the soul... In the care of our bodies, we must cooperate with Him.• Councils on Health, p.41

🙏🏽 *• A Point To Ponder •*
Taking care of our health is not just about physical well-being, but about spiritual vitality as well. • John Ortberg
_(FrontierOfHopeMinistry)_

21/05/2024

*A GOOD REPUTATION*

_Through their faith, the people in days of old earned a good reputation (Heb. 11:2, NLT)._

What do your neighbors say about you? Are you viewed as a person whose word is as good as gold? How valuable is your handshake? It is important to note a direct result of being faithful to God is the gift of a good reputation. *When you are faithful to God it correlates that you are faithful to other people as well.*
How does your spouse sees you? Pastor, how does your wife, children, and church members sees you.
Be careful though, it's easy to take pride in your reputation.

No wonder the wisest king says, "A good name is more desirable than great riches; to be esteemed is better than silver or gold" (Prov. 22:1). "Be more concerned with your character than your reputation, because your character is what you really are, while your reputation is merely what others think you are". ...
Let us treat others the way we want them treat us. Put a smile on someone's face today, and the Lord will shine His face upon you.

God bless you

21/05/2024

*TRUSTING GOD'S DELIVERANCE IN THE DARKEST OF VALLEYS*

*Psalm 23:4 "Even though I walk through the darkest valley, I will fear no evil, for you are with me; your rod and your staff, they comfort me."*

_We may find ourselves walking through the valley of the shadow of death—the darkest, most challenging moments that test our faith and resilience. It is in these moments that fear threatens to overpower us, but as believers, we have a powerful assurance: God saves His people._

*David understood this truth intimately. Despite facing trials and dangers throughout his life, he confidently declared, "I will fear no evil, for you are with me." David's unwavering trust in God enabled him to persevere through the darkest valleys.*

_When we encounter our own valleys, we must remember that God is with us. He walks beside us, leading and guiding us with His rod and staff. His presence brings comfort, assurance, and strength. He is our ever-watchful Shepherd, who will never leave us nor forsake us._

*God bless you *

Address

Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Owerengawe khala maso posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share